
在手机上保存,获得更好体验
Mtendere (Dmstry EDM Remix) - Molto Zambia
Lyrics by:Maxwell Msoni/Choolwe Siamubotu
Composed by:Choolwe Siamubotu
Kodi mu adziwa amfumu anu
Kodi mudziwa komwe muchokera
Ngati muna badwa akapolo
Kodi mu udziwa mtendere
Kodi mu adziwa amfumu anu
Kodi mudziwa komwe muchokera
Ngati muna badwa akapolo
Kodi mu udziwa mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Chimandi wawa ndi kaona anthu osoba kuchuluka
Timati bvuto ndi ana mwina ndi akulu ka
Ma bvalidwe osayenera kusamva kwa chuluka
A dube anati back to my roots iwe kumbuka
Ana auzyeni za kwao amveleko tu
Ayende kumudzi kwao aoneko tu
They learn about their ways aciteko do
Aoneko nyau nu bvina ngoma zili du du
Khalani guardian angelo mutetezi
Aphunzitseni zakwao ana A to Z
They learn about dos and don'ts ndi cite izi
Asa kule m'sinkhu tyala bembelezi
Sungani nwambo musataye mdambo
Dziwani cilankhulo chanu bambo
Know more about your heritage nwambo
Mhuuu miyambo
Kodi mu adziwa amfumu anu
Kodi mudziwa komwe muchokera
Ngati muna badwa akapolo
Kodi mu udziwa mtendere
Kodi mu adziwa amfumu anu
Kodi mudziwa komwe muchokera
Ngati muna badwa akapolo
Kodi mu udziwa mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Kodi mu'dziwa mtendere mtendere mtendere
Anati know where you are from
Udziwe tsogolo lako
Appreciate your mother tongue
Udziwe lokolo lako
Zitseko zonse zina sinkha
Uza khomololako
Minda zinasiya makolo
Nawe kololako
Ndine mwana m'ngoni osani sobeletsa
Ndingo bvina ingoma osani konkeleza
Ibangule mkango sinjenjemetsa
Kalindula nje no doc shebeleza
Mtunda wama ola uyamba ndi tente eii
Are you actually free or mwina ndi nthete eii
Tsiku uzapita kumalo ali chete eii
Akakonsha za we suzakhala chete eii
Can you become so passionate about
Your roots about your fruits
About your chiefs
Kings and queens and let it dominate
You can never know where
You are going nga sudziwa where you from
Conde ndili ndi konsho eyy
Kodi mu adziwa amfumu anu
Kodi mudziwa komwe muchokera
Ngati muna badwa akapolo
Kodi mu udziwa mtendere
Kodi mu adziwa amfumu anu
Kodi mudziwa komwe muchokera
Ngati muna badwa akapolo
Kodi mu udziwa mtendere
Kodi mu udziwa